eng
stringlengths
2
681
nya
stringlengths
1
797
This can make it easier to reach their hearts with Bible - based principles , motivating them to " fear the true God and keep his commandments . "
Zimenezi zingachititse kuti musavutike kuwafika pamtima mukamawaphunzitsa mfundo zamakhalidwe abwino za m 'Baibulo , kuwalimbikitsa ' kuopa Mulungu ndi kusunga malamulo ake . '
That , in turn , will give them added strength to keep on walking on the road to life " and not tire out . " - Isa .
Zimenezi zingawathandizenso kuti apitirize kuyenda ' mosatopa ' panjira yopita ku moyo . - Yes .
This brought anxiety . "
Zimenezi zinkatipatsa nkhaŵa . "
Susan summed up the account of her childhood experience by writing : " [ Al ] was to die only eight years later , by which time I was a committed atheist . "
Zimenezi zitachitika , mayi ake a Susan ananena kuti : ' N 'kutheka kuti ndi Mulungu amene wathandiza dokotalayu . '
How that word must have put her heart at ease !
Zimenezi ziyenera kuti zinam 'khazika mtima pansi mayiyu .
These too can retard growth in children .
Zimenezinso zimalepheretsa ana kukula bwinobwino .
How beautifully that is expressed !
Zimenezo zikulongosoledwa bwino chotani nanga !
That includes descriptions you may be familiar with - building houses and occupying them ; planting vineyards and eating the fruitage ; long enjoying the work of one 's hands ; a wolf and a lamb residing together ; and no harm occurring earth wide .
Zimenezo zikuphatikizapo mafotokozedwe amene mukudziŵa - kumanga nyumba ndi kukhalamo ; kuoka minda yamphesa ndi kudya zipatso zake ; kusangalala kwa nthaŵi yaitali ndi ntchito ya manja athu ; mmbulu ndi mwana wa nkhosa zidzakhala pamodzi ; ndipo dziko lonse lapansi silidzasakazidwa .
This is borne out by the following experience from Togo , West Africa .
Zimenezo zikusonyezedwa ndi nkhani iyi yochokera ku Togo , ku West Africa .
If he met the people 's demands , he , his family , and those of his court might have to cut back on some luxuries and make fewer demands on the people .
Zinali choncho chifukwa chakuti ngati akanachita zimene anthuwo anapempha , iye , banja lake ndiponso anthu ena okhala m 'nyumba ya mfumu sakanatha kupeza zinthu zapamwamba zimene anazolowera .
How sad that on this critical night , Jesus found himself having to remind them again what a Christian minister should truly be .
Zinali zomvetsa chisoni kwambiri kuti pausiku wofunika kwambiri umenewu , Yesu anayenera kuwakumbutsanso mmene mtumiki wachikristu ayenera kukhalira .
It would have been so easy to settle down in England , but after a short rest , I felt an obligation to return to my assignment .
Zinali zosavuta kukhazikika ku England , koma n 'tapuma kwakanthaŵi kochepa ndinaona kuti ndi bwino kubwereranso ku ntchito yanga ya umishonale .
That was a severe blow to Dad and to us children , aged from 8 to 19 .
Zinalitu zopweteka kwambiri kwa bambo komanso kwa ife ana a zaka zoyambira 8 mpaka 19 .
It warmed her heart to learn that God cares for all his sheep and sustains them through hard times .
Zinamukhudza mtima ataphunzira kuti Mulungu amasamalira nkhosa zake zonse ndipo amazithandiza pamavuto .
By coincidence , the company executive in charge of the trainees came by .
Zinangochitika kuti , bwana wa kampaniyo amene ankayang 'anira antchitowo anabwera ku ofesiko .
Coincidentally , just the week before , many had visited St .
Zinangochitika kuti mlungu umodzi wokha chikondwererochi chisanachitike , anthu zikwi zambiri anafika mu mzinda wa St .
It seemed as though everyone knew me already .
Zinangokhala ngati kuti aliyense akundidziŵa kale .
Understandably , the problem you identify may be different from that noted by your spouse .
Zingatheke kuti vuto limene mkazi kapena mwamuna wanu angatchule lingakhale losiyana ndi lanu .
Three Significant Differences
Zinthu Zitatu Zimene Zimasiyanitsa Aisiraeli ndi Akhristu
These and other factors have forced hundreds of millions in every corner of the earth to settle for substandard housing .
Zinthu ngati zimenezi pamodzi ndi zina , zapangitsa anthu mamiliyoni ambirimbiri padziko lonse kulolera kukhala m 'nyumba zimene si zabwino kwenikweni .
Speeding along in two 's or three 's , these futuristic vehicles used natural gas , which is cleaner than regular fuels .
Zinthu zamakono kwambirizi zinali kuyenda mofulumira pamzera , ndipo zinkakhala ziwiriziwiri kapena zitatuzitatu komanso zinkayendera gasi , chifukwa sawononga chilengedwe kwambiri pomuyerekezera ndi mafuta .
Progress has been made in such fields as transportation , health care , and communication .
Zinthu zapita patsogolo m 'zamayendedwe , kusamalira umoyo , ndi njira zolankhulirana .
Our ministry will be fruitful as we " recommend ourselves as God 's ministers . . . by kindness . " - 2 Cor .
Zinthu zidzatiyendera bwino mu utumiki ngati ' tikusonyeza kuti ndife atumiki a Mulungu mwa kukhala okoma mtima . ' - 2 Akor .
The events that Jesus mentioned - wars , earthquakes , pestilences , food shortages - would not be new in themselves .
Zinthu zimene Yesu anatchula monga nkhondo , zivomezi , miliri , njala , si zachilendo ayi .
Some ingredients are so toxic that it is illegal to dump them in a landfill .
Zinthu zina zosanganizidwa nzapoizoni kwambiri kwakuti ndi mlandu kuzitayira padzala .
Inexorably , these life - sustaining essentials are being either contaminated or whittled away - by man himself .
Zinthu zochirikiza moyo zofunika zimenezi zikuipitsidwa kapena kuchepetsedwa mosaleka - ndi munthu mwini .
The items marked " ? "
Zinthu zolembedwapo " ? "
The dangers are real !
Zinthu zoterezi zilipodi .
When feeling romantic , a pair may even perform a duet to confirm their attachment to each other .
Zitakondana , yaimuna ndi yaikazi zimaimbira pamodzi kutsimikiza kuti sizidzasiyana .
Shortly afterward , I started experiencing constant excruciating pain and frequent urination ( 50 to 60 times a day ) .
Zitangochitika izi , ndinayamba kumva ululu waukulu nthaŵi zonse ndipo ndinkakodza pafupipafupi ( maulendo 50 kapena 60 patsiku ) .
Boaz married Ruth .
Zitatere , Boazi anakwatira Rute .
The examples of Hezekiah , Hannah , and Jonah also teach us a vital lesson about what we should not fail to remember as we pray while under duress .
Zitsanzo za Hezekiya , Hana ndiponso Yona zimatiphunzitsa chinthu china chimene tiyenera kukumbukira tikamapemphera za vuto limene tili nalo .
How vividly these examples teach us to listen to the counsel of those whom Jehovah uses in positions of responsibility and to respect them !
Zitsanzo zimenezi zikutiphunzitsa bwino kumvera uphungu wa anthu amene Yehova akuwagwiritsa ntchito pa maudindo ndiponso kuwalemekeza .
They must also be achievable and realistic .
Ziyeneranso kukhala zotheka ndiponso zoti tingakwanitse .
Self - Imposed Trials
Ziyeso Zodzibweretsera Tokha
Some Warning Signs of Mental Disorders
Zizindikiro Zina Zimene Zingasonyeze Kuti Munthu Angadwale Matenda a Misala
Statistics show that the economic division between rich and poor has become a chasm .
Ziŵerengero zimasonyeza kuti kusiyana m 'zachuma pakati pa olemera ndi osauka kwakhala kwakukulu koposa .
Other activities and concerns are less important or even vain .
Zochita zina ndi nkhaŵa zina sizili zofunika kwenikweni mwinanso nkukhala zopanda pake .
Some historical background will help us to see how present - day conflicts go back to World War I .
Zochitika za m 'mbiri zidzatithandiza kuona mmene kulimbana kwamakonoku kulili kogwirizana ndi Nkhondo Yadziko I .
The incidents related in Numbers show how easily those who neglect their spirituality can fall into wrongdoing , such as murmuring , immorality , and idolatry .
Zochitika zimene zafotokozedwa m 'buku la Numeri zimasonyeza mmene zilili zosavuta kuti anthu amene amanyalanyaza zinthu zauzimu achite choipa , monga kung 'ung 'udza , chisembwere , ndi kulambira mafano .
Such features amount to evidence of an organization .
Zochitika zonsezi zimachitira umboni kuti pali gulu .
Blush can highlight your cheekbones .
Zofiiritsa masaya zingakometsere mafupa anu a m 'masaya .
Their record shows that it is folly to trust in imperfect humans .
Zolembera zawo zimasonyeza kuti chiri chopusa kukhulupirira mwa anthu opanda ungwiro .
All that Ezra relates in First Chronicles must surely have benefited the Israelites , helping them to renew their zeal for Jehovah 's worship at the temple .
Zonse zimene Ezara anafotokoza m 'buku Loyamba la Mbiri ziyenera kuti zinapindulitsa Aisrayeli . Zinawathandiza kukhalanso achangu polambira Yehova pakachisi .
All of these are forms of dishonesty .
Zonsezi ndi njira za kusaona mtima .
How all of this encourages anointed ones as well as their associates in Jehovah 's service , who hope to live on a paradise earth !
Zonsezi zimalimbikitsa odzozedwa komanso anzawo amene akugwira nawo ntchito mu utumiki wa Yehova , amene akuyembekezera kudzakhala ndi moyo padziko lapansi la paradaiso !
The greatest Giver of all , of course , is our Creator , Jehovah God .
Zoonadi , Mpatsi wamkulu kuposa onse ndiye Mlengi wathu , Yehova Mulungu .
True , Jehovah has endowed us with a measure of intelligence and a conscience to help us to discern right from wrong .
Zoonadi , Yehova anatipatsa nzeru ndi chikumbumtima pamlingo winawake kuti zitithandize kuzindikira chabwino ndi choipa .
Yes , he can use imperfect humans to do great works despite their weaknesses .
Zoonadi , iye amagwiritsa ntchito anthu opanda ungwiro kuchita zazikulu ngakhale kuti iwo ali ndi zofooka .
Yes , you can develop the inner strength to face any situation in life .
Zoonadi , mukhoza kukhala ndi mphamvu zokuthandizani kulimbana ndi chilichonse pamoyo wanu .
Of course , you might think that this is an extreme example and that Conan Doyle was more foolish than you would ever be .
Zoonadi , mungaganize kuti chimenechi chili chitsanzo chopambanitsa ndi kuti Conan Doyle anali wopusa kwambiri kuposa mmene mungakhalire .
Really , although no one today can perform cures like these , we can be confident that under God 's rule mankind will be elevated to perfection , healed of all mental and physical diseases .
Zoonadi , ngakhale kuti palibe aliyense lerolino amene angachiritse motero , tingathe kukhala ndi chikhulupiriro kuti pansi pa ulamuliro wa Mulungu anthu adzafika ku ungwiro , adzachiritsidwa matenda awo onse akuthupi ndi amalingaliro .
Yes , various factors contribute to happiness , such as cultivating friendship with God and with his people , trusting in Jehovah implicitly , accepting his divine counsel , and being considerate of others .
Zoonadi , zinthu zosiyanasiyana zimabweretsa chimwemwe . Zinthu zake ndi monga kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu ndi anthu ake , kukhulupirira Yehova ndi mtima wonse , kumvera malangizo ake , ndi kusamalira anthu ena .
Causes of Ill Manners
Zopangitsa za Mayendedwe Oipa
Harmless Fun or Mental Poison ?
Zosangulutsa Zosavulaza Kapena Paizoni ya Maganizo ?
Such episodes can occur hundreds of times each night and cause a child to feel exhausted upon awakening .
Zoterezi zimatha kuchitika kambirimbiri usiku uliwonse ndipo zikamatero zimam 'pangitsa mwana kudzuka ali wotopa kwambiri .
Dwell on What Jehovah Has Done for You , 1 / 15
Zoti Achinyamata Achite , 1 / 1 , 3 / 1 , 5 / 1 , 7 / 1 , 9 / 1 , 11 / 1
The bitter fruits of corruption remind us of King Solomon 's words : " I myself returned that I might see all the acts of oppression that are being done under the sun , and , look ! the tears of those being oppressed , but they had no comforter ; and on the side of their oppressors there was power , so that they had no comforter . " - Ecclesiastes 4 : 1 .
Zotulukapo zopweteka za kusaona mtima zimatikumbutsa za mawu a Mfumu Solomo : " Ndinabweranso tsono ndi kupenyera nsautso zonse zimachitidwa kunja kuno ; ndipo taona , misozi ya otsenderezedwa , koma analibe wakuwatonthoza ; ndipo akuwatsendereza anali ndi mphamvu koma iwowa analibe wakuwatonthoza . " - Mlaliki 4 : 1 .
Global Efforts to Bring Peace
Zoyesayesa za Padziko Lonse Zodzetsa Mtendere
The miracles they performed would make many of the householders eager to meet Jesus and listen to his Kingdom message . - 7 / 1 , pages 16 - 17 .
Zozizwitsa zimene iwo anazipanga zikapanga eninyumba ambiri kukhala ofunitsitsa kukumana ndi Yesu ndi kumvetsera ku uthenga wake wa Ufumu . - 7 / 1 , masamba 16 - 17 .
[ Box / Picture on page 23 ]
[ Bokosi / Chithunzi patsamba 23 ]
[ Box / Pictures on page 7 ]
[ Bokosi / Zithunzi patsamba 17 ]
[ Box / Pictures on page 9 ]
[ Bokosi / Zithunzi patsamba 25 ]
[ Box / Pictures on page 28 ]
[ Bokosi / Zithunzi patsamba 28 ]
[ Box on page 16 , 17 ]
[ Bokosi pamasamba 16 , 17 ]
[ Box / Pictures on page 10 ]
[ Bokosi patsamba 10 ]
[ Box on page 17 ]
[ Chithunzi patsamba 17 ]
[ Picture on page 16 ]
[ Chithunzi patsamba 19 ]
[ Picture on page 17 ]
[ Chithunzi patsamba 30 ]
[ Blurb on page 7 ]
[ Mawu Otsindika patsamba 25 ]
self - centered .
amakhala wodzikonda .
" Hey , " one of them yelled , " that 's him .
anafuula motero mmodzi wa iwo , " ndiuja akupita paja .
The Bible 's View
imodzi yokha , ndidzam 'pangirawom 'thangatira
Tlapanec is just one of the 17 Indian languages in Mexico in which the brochure You Can Be God 's Friend !
kamapezeka m 'zinenero zokwana 17 zimene anthu achimwenye amene amakhala ku Mexico amalankhula .
or , ' What are we to put on ? ' "
kapena , Tidzavala chiyani ? "
was released at the end of this talk .
linatulutsidwa pamapeto a nkhaniyi .
magazines have occasionally featured articles that help us to combat discouragement .
nthaŵi zina afalitsa nkhani zimene zingatithandize kulimbana ndi kukhumudwa .
○ Zephaniah 3 : 9 - A common human language does not guarantee unity , as is shown by the wars fought between people of the same tongue .
o Zefaniya 3 : 9 - Chinenero chofala cha munthu sichimatsimikizira chigwirizano , monga momwe zasonyezedwera ndi nkhondo zomenyedwa pakati pa anthu a chinenero chimodzi .
Research
olakwika ?
for they will all of them know me . . .
pakuti iwo onse adzandidziŵa . . .
For a discussion of the effects of unwed motherhood on young women , see the article " Young People Ask . . .
wa May 8 , 1986 pa mutu wakuti " Achichepere Akufunsa . . .
someone might ask .
wina angafunse motero .
• " The seventh one in line from Adam , Enoch , prophesied also regarding [ the wicked ] . " - JUDE 14 .
• " Inoke , wa m 'badwo wachisanu ndi chiwiri kuchokera kwa Adamu , ananenera za [ anthu oipa ] . " - YUDA 14 .
□ " You must love Jehovah your God with your whole heart and with your whole soul and with your whole mind . " - Matthew 22 : 37 .
□ " Udzikonda Ambuye Mulungu wako ndi mtima wako wonse , ndi moyo wako wonse ndi nzeru zako zonse . " - Mateyu 22 : 37 .
□ How have " the things in the heavens " and " the things on the earth " been gathered together in the Christ ?
□ Kodi zinthu " za kumwamba " ndi " za padziko " zasonkhanitsidwa motani mwa Kristu ?
□ On her wedding day , a bride carefully arranges her wedding ensemble so that it includes " something old , something new , something borrowed , and something blue . "
□ Patsiku la ukwati , mkwati amalinganiza mosamala zovala zake za paukwati kotero kuti pakhale " zina zakale , zina zatsopano , zina zobwereka , ndi zina zabuluwu ndipo amakhulupirira kuti akatero adzakhala ndi ukwati wabwino . "
▪ Between the fifth and ninth months of life , babies generally start to need more calories and proteins than milk provides .
▪ Kuyambira mwezi wa faifi mpaka wa naini , mwana amafunikira zakudya zambiri zopatsa mphamvu ndi zomanga thupi kuposa zimene angazipeze mu mkaka wa m 'maere .
■ In the area of Tullamore , the Witnesses had Bible discussions with a woman named Jean over a period of seven years .
▪ M 'dera la Tullamore , Mboni zinakambitsirana za Baibulo ndi mkazi wina wotchedwa Jean kwa nyengo yoposa zaka zisanu ndi ziŵiri .
◆ How does the presiding officer acknowledge Jesus ' healing ability , yet how does Jesus expose the man 's hypocrisy ?
◆ Ndimotani mmene mkulu akuvomerezera kuthekera kwa kuchiritsa kwa Yesu , komabe ndimotani mmene Yesu akuvumbulira chinyengo cha munthu ?