Chichewa
stringlengths
10
500
emotion
stringclasses
7 values
"Omwe unapangana nawo chipangano kenako naaswa chipangano chawo panthawi iliyonse (imene mwapangana), ndiponso iwo saopa Allah.
fear
Ndipo amene angamenye nkhondo pa njira ya Allah, kenako ndikuphedwa kapena kupambana tidzampatsa malipiro aakulu.
joy
"Tero ndithu tikadakulawitsa chilango chachikulu cha moyo (wa pa dziko lapansi) ndi chilango chachikulu utafa; kenako siukadapeza mthandizi wokupulumutsa kwa Ife.
disgust
Iwo ali ndi ana aamuna anayi, ndipo onse ali m'choonadi.
neutral
Tero, Allah waikhotetsa mitima yawo chifukwa chakuti iwo ndi anthu osazindikira.
disgust
Kenako anayankha kuti: "Inde, amunawo anabweradi kwa ine, koma sindinadziwe kuti achokera kuti.
surprise
Iye akuti: "Njoka inu, obadwa inu a mamba, mudzatha bwanji kuthaŵa kulanga kwake kwa gehena?"
fear
Ndipo Mbuye wako wakwana kukhala muongoli ndi mthandizi (wako).
neutral
Timasonyezanso kuti tikutsanzira chikhulupiriro cha Yosefe komanso kuti tikutsanzira Yehova, yemwe ndi wachifundo.
neutral
"Allah adzati: "Ili ndi tsiku lomwe olankhula zoona kudzawathandiza kuona kwawo.
neutral
Ndipo amene adachita zoipa, phokoso lidawachotsa moyo, tero kudawachera m'nyumba zawo ali lambilambi (atafa).
anger
Waphunzitsa munthu zinthu (Zambiri) zomwe (iye) sadali Kuzidziwa.
disgust
Michael Lidzakhala dzina lake ngati adabadwira ku France.
neutral
Tilandireni (ntchito yathuyi), ndithudi, Inu ndinu Akumva; Odziwa."
neutral
"Ndipo tsiku la Qiyâma udzawaona omwe adamnamizira Allah, nkhope zawo zili zakuda.
disgust
Sanakumbukira dzanja lake, tsikuli anawawombola kwa msautsi.
neutral
Kapena mudafuna kuti mkwiyo ukutsikireni kuchokera kwa Mbuye wanu; tero mwaswa lonjezo langa"?
anger
Tikuwalipirira anthu osalungama.
anger
Sinditsatira Koma zokhazo zimene zikuvumbulutsidwa Kwa ine; ndipo ine sindili kanthu koma Mchenjezi wolongosola (Zofunika) ."
disgust
Sinditsatira koma zokhazo zimene zikuvumbulutsidwa kwa ine; ndipo ine sindili kanthu koma mchenjezi wolongosola (zofunika)."
disgust
Ndipo mulole iwo kuonjezera mu unyinji kudutsa dziko lapansi. "
neutral
Ndikuganiza kuti ziyenera kukhala patsamba la aliyense, Patric.
neutral
Ndikuti usiku umenewo ngwabwino kuposa miyezi chikwi chimodzi.
neutral
"Moyo wa pa dziko lapansi wakometsedwa kwa amene sadakhulupirire, ndipo amawachitira chipongwe amene akhulupirira.
neutral
""Ndipo tadza kwa iwe ndi (chinthu) choonadicho, ndithu ife ndi owona (pazimene tinenazi)."
neutral
(Mneneri Mûsa) adati: "Ndithudi, inu ndinu anthu osazindikira."
disgust
Kodi mukutsutsana naye (Mthenga wa Mulungu) pazimene adaziona.
anger
Ndipo ndalamulidwa kukhala mmodzi wa okhulupirira."
neutral
(Luti) adati: "Ndithudi, inu
neutral
Koma sizinthu zakumwamba, mwachitsanzo, angelo, gawo la chilengedwe.
neutral
Chamunthu) ndi wosaumbidwa,
disgust
" (Iblis) adanena: "Ine ndine wabwino kuposa iye (Adam); chifukwa ine mudandilenga kuchokera ku Moto, ndipo iye mudamulenga kuchokera kudongo."
neutral
koma njira ya munthu wolungama ili ngati msewu waukulu.
neutral
ndipo anthu olungama adzaona nkhope yake.
neutral
Ndipo ine sindingathamangitse amene akhulupirira (monga momwe mudandipemphera kuti ndiwathamangitse anthu ofooka kuti inu mulowe m'malo mwawo), ndithu iwo adzakumana ndi Mbuye wawo, ndipo ine ndikukuonani monga anthu osazindikira (mbuli)."
disgust
Koma pamene (pakatipo) padalemera (patangotsala pang'ono kuti abereke) anampempha Allah, Mbuye wawo (kuti): "Ngati mutipatsa mwana wabwino, ndithu tidzakhala mwa othokoza kwambiri."
neutral
Muolowetsa dzanja lanu, nimukwaniritsira zamoyo zonse chokhumba chawo."
neutral
"Ndipo musakhale monga aja achinyengo omwe akunena: "Tamva (choonadi ndipo tachisunga)," pomwe iwo sakumva (kumva kochigonjera).
neutral
"Ndipo masautso akampeza munthu, amapempha Mbuye wake ndi kutembenukira kwa Iye (pomwe chikhalirecho adali kumnyoza).
neutral
Mariya anati: 'Kodi zimenezi zingatheke bwanji?
surprise
Mafunso aliwonse atha kupita ku Federal Protective Service. "
neutral
Ndidzakhala naye m'nthawi ya masautso."
fear
Koma Allah akufuna kuchitsimikiza choonadi ndi mawu Ake ndi kudula mizu ya osakhulupirira, (pomenyana ndi gulu lamphamvulo, omwe ndi ankhondo a Chikuraishi).
neutral
Nena: "Utsogozi weniweni ngwa Allah, ndipo talamulidwa kuti tigonjere Mbuye wa zolengedwa zonse."
neutral
Iye anati: "Njoka inu, ana a mphiri, mudzathawa bwanji chiweruzo cha Gehena?"
fear
Ndipo ine ndine mmodzi mwa Asilamu (omugonjera monga iwo akumgonjera)."
joy
Fanizo la mkazi ndi ndalama yotayika likutiuza chochita.
neutral
Ndipo tidampatsa nzeru ali mwana.
neutral
Ndipo pa munthu: Zimachotsa madalitso a moyo wa munthu,
disgust
Anali atalonjeza kuti adzapangitsa kuti ana a Yakobo akhale mtundu waukulu.
neutral
Nena (kwa iwo): "Zimene zili kwa Allah nzabwino kwa inu kuposa masewero ndi malonda.
neutral
"Sad, ndikulumbira Qur'an (iyi) ya ulaliki (wothandiza).
disgust
Iye (Allah) sakonda opyoza muyeso (oononga).
disgust
"Choncho ndidati (kwa anthu anga): Pemphani kwa Mbuye wanu chikhululuko (pa kukana kwanu ndi kutonza kwanu), ndithu Iye ali Wokhululuka kwambiri.
sadness
Tikhoza kungokhudza mitu yochepa yokha m'mawa uno yokhudza Kristu Yesu Mwini.
neutral
"Ndipo (Mûsa) pamene adakula nsinkhu wake ndi kulingana bwino tidampatsa nzeru ndi maphunziro.
neutral
""Atsateni omwe sakupemphani malipiro (pa kukulangizani kwawo), ndipo iwo ngoongoka."
neutral
Choncho, nena: "Kodi bwanji simukumuopa?"
fear
"Asiye azidya (chakudya monga momwe zidyera nyama) ndi kusangalala; ndipo chiyembekezo chiziwatangwanitsa ndi kuwanyenga; posachedwa adziwa (kuti zimene amaziyembekezerazo nzabodza).
neutral
Kodi iye angafanane ndi yemwe akulamula mwa chilungamo, yemwenso ali pa njira yolunjika?
neutral
Otsalira adzatembenuzira kumbuyo, otsalira a Yakobo, kwa Mulungu Wamphamvu.
neutral
" (Ayuda) sangamenyane ndi inu ali pa gulu kupatula m'midzi yotetezedwa ndi malinga, kapena kuseri kwa zipupa.
neutral
"Pamene adawauza Nuh m'bale wawo kuti: "Kodi simukuopa (Allah ngakhale nditakuuzani zoopsa zimene zikukudikirani)?"
fear
Yakobo ankayesetsa kuchita zonse zimene akanatha kuti adalitsidwe ndi Mulungu ngakhale kuti ankakumana ndi mavuto ena.
neutral
Friday wabwino News wabwino kwa ochimwa monga inu ndi ine.
joy
Nakuti ule omwe an'bzicepsa pakati panupa, umweyo ndiye nkulu."
neutral
Ndithu Allah akufuna kuwalanga ndi zimenezo pa dziko lapansi, ndi kuti mizimu yawo ichoke ali osakhulupirira.
anger
Ndithu nzoipa kwabasi zomwe iwo akhala akuchita.
disgust
"Kodi akuganiza kuti tikamawapatsa chuma ndi ana,
neutral
Tsiku lakudza zina mwa zizindikiro za Mbuye wako, munthu (wosakhulupirira) chikhulupiliro chake (panthawiyo) sichidzamthandiza, yemwe sadakhulupirirepo kale, kapena (msilamu) yemwe sanapindule nacho chikhulupiliro chake.
neutral
Ndipo ndithu lonjezo lanu ndi lowona, Ndipo Inu ndi oweruza mwachowonadi kuposa aweruzi onse."
neutral
Ndithu, Ife tamlenga munthu kuchokera Kumbewu ya umunthu yosanganikirana (Ya mkazi ndi ya mwamuna) kuti Timuyese mayeso (ndi malamulo Athu); Choncho tidampanga kukhala wakumva Ndi wopenya; (amve mawu a Mulungu) Ndi kuti aone zisonyezo Zake).
neutral
Palibe ayenera kupulumutsidwa ndi kubwezeretsedwa kwa Mulungu, kotero Iye anali wachisomo kuombola anthu ku Israel.
neutral
"Ndipo akadayesa kumenyana nanu amene sadakhulupirire; akadatembenuza misana kuthawa; kenako sakadapeza mthandizi kapena mtetezi.
neutral
Iyi ndi sura; Taivumbulutsa,
neutral
Kodi wadya zipatso za mtengo umene ndinakulamulira kuti usadye?"
disgust
Ndipo ngati anyozera dziwa kuti Allah afuna kuwapatsa chilango cha ena mwa machimo awo.
anger
Munthu adzanena tsiku limenelo: "Nkuti kothawira (chilangochi?) "
neutral
Ndiye kuti palibe chomwe chatsala, koma zonse ndi za mthenga.
neutral
Nena: "Allah ndi Yemwe akuyambitsa zolengedwa kenaka ndi kuzibweza (pambuyo poonongeka).
neutral
" (Farawo) adati: "Inde, (ndipo kuonjezera apo) ndithu inu mudzakhala mwa amene amakhala pafupi (ndi ine, monga nduna zanga)."
neutral
Zedi, zitsanzo adzapelekedwa mlanduwo zitsanzo 'ndi zingati mthenga mwa inu.
surprise
"Nena: "Simudzafunsidwa pa zimene (ife) talakwa, nafenso sitidzafunsidwa pazimene mukuchita."
fear
Taonani, mapazi a iwo amene adayika mwamuna wako ali pakhomo, ndipo adzakunyamula iwe kuchokera!"
anger
Kodi bwanji sadatumizidwe mngelo kwa iye kuti azikhala naye limodzi uku akuchenjeza?"
surprise
Ndipamene ndinawatsekereza ana a Israyeli kwa iwe (kuti asakuzunze) pamene udawadzera ndi zisonyezo zooneka, ndipo aja mwa iwo omwe sadakhulupirire, adati: "Ichi sichina, koma ndi matsenga owonekera."
neutral
Choncho mdzadziwa mmene lilili chenjezo Langa (pa inu).
neutral
"Kapena tidawapatsa buku lina tisadapereke ili, kotero kuti iwo agwiritsitsa limenelo (ndi kugwirizana nazo zili mmenemo)?
neutral
Ngati utichotsera chilangochi, ndithudi tikukhulupirira, ndipo tiwatumiza pamodzi nawe ana a Israyeli (kuti unke nawo kumene ukufuna)."
neutral
Ndithudi, zimene zavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Mbuye wako, ziwaonjezera ambiri a iwo (Ayuda) kulumpha malire ndi kusakhulupirira.
neutral
"Ndipo ikawerengedwa kwa iwo Qur'an, sagwetsa pansi nkhope zawo (modzichepetsa).
neutral
"Ndipo sikotheka Qur'an iyi kukhala yopekedwa, yosachokera kwa Allah (monga momwe munenera).
neutral
munthu zinthu zomwe sadali kuzidziwa,
disgust
Mwachitsanzo, ku Andorra pazifukwa zina simungathe kupha anthu oposa awiri patsiku.
neutral
mtengezereni njira iye atsupaye dzulu ya maingu,
neutral
Ndiyeno iyo idzafika kumapeto a moyo wake ndipo sipadzapezeka woithandiza."
anger
Kodi munganene bwanji zamwano chotere kwa ine?"
anger
"Kapena muli nawo mapangano ndi Ife okafika mpaka tsiku lachimaliziro akuti inu mudzapeza zimene mukudziweruzira?
neutral
Ndipo ndithu Allah ali pamodzi ndi ochita zabwino.
neutral
" (Ndipo tidzawauza) "Lowani m'menemo mwamtendere, mosatekeseka."
neutral