Chichewa
stringlengths
10
500
emotion
stringclasses
7 values
Kenako tinaona kalavani inayake yakutha.
disgust
Ndikuganiza kuti ukunena zowona, Aaron.
neutral
"Ndipo akutiponyera fanizo (lotsutsa kukhoza Kwathu kuukitsa akufa) ndi kuiwala chilengedwe chake (chochokera kumadzi opanda pake).
disgust
Koma dziwani izi: Mukandipha, mudzakhala mukupha munthu wosalakwa.'
anger
Kodi nanunso mwapeza zomwe Mbuye wanu adakulonjezani kuti nzoona?"
neutral
"Koma amene angafune (zina) kusiya zimenezi iwowo ndiwo olumpha malire.
disgust
Tipatsirenitu gawo la chilango chathu lisanafike tsiku lachiwerengero."
anger
Ndipo akakapempha chithandizo (chifukwa cha ludzu loopsya lomwe likawapeza), akathandizidwa popatsidwa madzi (otentha kwambiri) monga madzi a chitsulo chosungunuka, omwe adzasupula nkhope zawo.
disgust
Pakuti dzanja lanu linali kundilemera usana ndi usiku."
fear
Yemwe angakhale connected ndi Qur'an, akhala wolemekezeka kuposa wina aliyense, chifukwa Allah analemekeza chilichonse chokhudzana ndi Qur'an.
neutral
Ndipo posachedwa adzawalipira pa zomwe adali kupeka.
anger
Kumbukirani kuti analemba kuti: "Mulungu ali wamkulu woposa mitima yathu."
neutral
Pamapeto pa tsiku, banja liyenera kuiwala zonse - a Mark V. Olson.
sadness
"Kodi akukulonjezani kuti mukadzafa ndikusanduka dothi ndi mafupa, mudzaukitsidwanso (m'manda)?
disgust
Ndiye dzifunseni kuti, 'Kodi n'kutheka kuti Mulungu akugwiritsa ntchito anthu amenewa pofuna kundikokera kwa iye?'
neutral
"Sipadzakhala (china) koma mkuwe umodzi basi; adzangozindikira iwo onse atabweretsedwa patsogolo Pathu.
neutral
Iye anati: "Ndachita pangano ndi maso anga.
neutral
Kodi kunyumba kwa bambo ako kuli malo oti tikhoza kugonako?"
neutral
ndipo wolungama akhale motetezedwa.
neutral
Nena: "Zozizwitsa zili kwa Allah; ndipo ine ndine mchenjezi woonekera, (ndilibe mphamvu zokudzetserani zozizwitsa koma pokhapo Allah atafuna)."
neutral
Ndipo wawaikira nthawi (yodziwika) yopanda chikaiko, (yowaukitsira ku imfa).
sadness
"Kodi zidzakhala zotani pamene tidzawasonkhanitsa tsiku lopanda chikaiko?
neutral
"Kapena iwo ali nawo othandidzana nawo (pa mau awa)?
neutral
Onse adzabwerera kwa Ife.
neutral
Adzabwerera tsiku la nkhondo.
neutral
Ndipo amene atembenukire kutali (kunyoza iwe, ndiye kuti zoipa zili pa iye mwini).
anger
" (Nena:) "Kodi ndifune woweruza wina kusiya Allah, pomwe Iye ndi Yemwe adavumbulutsa buku kwa inu lofotokoza chilichonse?"
fear
"Kuti liwachenjeze amene ali moyo, ndi kuti litsimikizike liwu (la chilango) pa osakhulupirira.
fear
Ndipo anthu untamed adzalowa izo, ndipo iwo aiipitse.
disgust
"Basi, kumbutsa (anthu) ndithu iwe, ndiwe mkumbutsi.
neutral
Komabe, "ikapezedwa idzabwezera kasanu ndi kaŵiri; idzapereka chuma chonse cha m'nyumba yake."
anger
Zinali zosatheka, zinali m'magazi anga.
surprise
Kodi munthu akuganiza kuti Ife (Amene tidamlenga kuchokera Popanda chilichonse) sitidzatha Kusonkhanitsa mafupa ake (ofumbwa)?
disgust
"Ndipo ndithu alipo ena mwa inu otsalira m'mbuyo sapita ku nkhondo, (ndiponso amaletsa anzawo).
neutral
"Naipereka kwa iwo (koma sadadye); iye adanena (modabwa): "Kodi bwanji simukudya?"
anger
"Ndithu Ine ndine Allah palibe wopembedzedwa mwachoonadi koma Ine; choncho ndipembeze, pemphera Swala moyenera pondikumbukira.
joy
Ndipo mwaphunzitsidwa (ndi iyi Qur'an) zomwe simudali kuzidziwa, inu ngakhale makolo anu.
neutral
Ndiyendetseni m'njira yoona,
neutral
Koma osadandaula, Lena, zomwe ndidakwanitsabe kuwombera.
fear
Pakuti ndaona kuti mukhale basi pamaso panga, mkati m'badwo uno.
anger
Davide anali ndi zinthu zonsezi koma anakhala wodzichepetsa kwa moyo wake wonse.
neutral
Kapena yochokera Dead kapena Alive.
neutral
"Ndipo iwo akadakhulupirira nadzitchinjiriza (ku zoletsedwa), ndithudi, mphoto yochokera kwa Allah ikadakhala yabwino kwa iwo, akadadziwa.
neutral
Unali wangwiro m'njira zako chilengedwere iwe, mpaka chinapezeka mwa iwe chosalungama.
anger
Koma popeza pa nthawiyi n'kuti dzina la Mulungu likudziwika kale, n'chifukwa chiyani Mose anafunsa funso limeneli?
neutral
"Ndithu amene adzadze kwa Mbuye wake uku ali wamachimo, adzapeza moto wa Jahannam; sadzafa m'menemo, ndipo sadzakhalanso ndi moyo wabwino.
sadness
Kodi ukuona chifukwa chake Mulungu anawononga anthuwo? - Iwo anali oipa, ndipo zimene ankaganiza zinali 'zoipa zokhazokha.'
disgust
"Akukufunsa za mowa ndi njuga.
neutral
Cifukwa cace, taonani, nditumiza kwa inu aneneri ndi anzeru ndi alembi.
neutral
"Adati: "Sichina ichi (Qur'an) koma ndi matsenga amene adalandiridwa (kuchokera kwa amatsenga akale),
neutral
mu maina Ake Iye Wapamwambamwamba,
disgust
Ngati akadamumvera Allah, ndithu zikadakhala zabwino kwa iwo.
neutral
"Auze amene sadakhulupirire: "Posachedwapa mugonjetsedwa ndi kusonkhanitsidwa ndi kuponyedwa ku Moto.
fear
Iye anayankha kuti: "Inde, ndifedi Akristu chifukwa chakuti Yesu ndiye chitsanzo chathu.
neutral
Taonani, adzailowa kwa inu, ndipo mudzaona njira yawo ndi zimene anachita.
neutral
"M'nthaka muli zizindikiro kwa otsimikiza, (zosonyeza kuti Allah alipo).
neutral
""Pita ndi kalata yangayi, kaiponye kwa iwo; kenako ukadzipatule kwa iwo (ukakhale pambali) ndi kuona momwe azikayankhira."
neutral
Tsoka inu, chifukwa muli ngati manda achikumbutso osaonekera, moti anthu amayenda pamwamba pake koma osadziwa!"
disgust
Ngati utsata zilakolako zawo pambuyo pa zomwe zakudzera, monga kuzindikira (kwenikweni), sudzapeza mtetezi aliyense ngakhale mthandizi kwa Allah.
neutral
Panopa Satana akuukira kwambiri anthu a Mulungu.
disgust
(Akawauza kuti): "Ndithu iyi ndi mphoto
joy
Ndipo kum'bandakucha, iwo Amapempha chikhululuko.
sadness
Tikatero, mnzathuyo sadzavutika kutimvetsera.
neutral
Ndipo pamene mukuwapatsa chuma chawo, funani mboni (zoonelera kuperekedwa kwa chumacho).
anger
"Komanso wochitira zabwino makolo ake ndipo sadali wodzitukumula (kwa anthu) kapena kunyoza (Allah).
neutral
"Choncho apewe (osakhulupirirawa) amene anyozera chikumbutso Chathu (Qur'an); ndipo palibe chimene akufuna koma moyo wa padziko lapansi basi.
neutral
Sindinawauze amayi ako zokwanira; Ndikanayenera kumamuuza tsiku lililonse chifukwa anali wangwiro tsiku lililonse.
neutral
Nena: "Nanga bwanji simukumuopa?"
fear
Mtima wake wakhazikika, sadzaopa, kufikira adzaona adani ake.
fear
Perekani chitsanzo cha "zakuya za Mulungu" zomwe gulu la kapolo lazifotokoza.
neutral
Kapena kudza zina mwa zizindikiro za Mbuye wako (zomwe adati zidzadza)?
neutral
"Ndipo adatuluka kuchipinda chopemphelera ndikuonekera kwa anthu ake, ndipo adawalozera (pomwe sadathe kuyankhula) kuti: "Lemekezani Allah m'mawa ndi madzulo."
neutral
""Ndipo Allah achilimbikitsa choonadi ndi mau Ake, ngakhale oipa anyansidwe nazo."
anger
Mtsikana akhoza kukhala ndipo adzatchedwa yemweyo - Nastya.
neutral
pa dziko ndithudi umenewo ukuchokera kwa Iye Subhaanahu Wataalaa.
neutral
Kodi iwe ukuganiza kuti mwa aŵiriŵa ndani anasangalatsa Mulungu?
neutral
Ndimasulireni maloto angawa, ngati inu mumatha kumasulira maloto."
neutral
"Ena mwa inu mwawawona kale 'alonda athu apamwamba' kale.
neutral
""Ndithu takhulupirira Mbuye wathu kuti atikhululukire zolakwa zathu ndi matsenga amene watikakamiza (kuchita); ndipo Allah ndi Yemwe ali Wabwino ndi Wamuyaya (osati iwe)."
neutral
Ndipo taika chidani ndi kusakondana pakati pawo mpaka tsiku la chimariziro.
anger
Ngati anamva zimenezi Dhamma, adzakhala ndi mwamsanga anamvetsa izo.'
neutral
"Kodi sadaone kuti (mwana wang'ombe) sabweza mawu kwa iwo, ndiponso sangathe kudzetsa matsautso kwa iwo ngakhale zothandiza.
disgust
Mngelo amene analankhula ndi Yosefe anati: "Adzapulumutsa anthu ake ku machimo awo."
neutral
""Ndipo tikukhazikani (inu) pambuyo pawo m'dzikomo.
neutral
Limatiuza dzina la mkazi wake ndiponso mayina a ena mwa ana ake.
neutral
Ndipo chikadza chipulumutso chochokera kwa Mbuye wako amanena: "Ndithu ife tidali pamodzi ndi inu."
neutral
kwa anthu a dziko lino amene mphotho yawo ili mʼmoyo uno.
joy
Koma chofunika kwambiri n'chakuti zimene tinkachita pa nthawiyi zinathandiza kuti tilimbitse ubwenzi wathu ndi Mulungu komanso kuti ine ndi mkazi wanga tizigwirizana kwambiri."
neutral
"Nena: "Kodi nthaka njayani ndi zomwe zili m'menemo, ngati inu mukudziwa (kanthu)!"
neutral
Izo ndi zosangalatsa za moyo wa dziko lapansi (zomwe sizili kanthu).
joy
Ndipo kodi njokayo ndi ndaninso yoti n'kukayikira chilungamo cha mawu a Mulungu ndi mawu a mwamuna wake?
disgust
Solomo anali ndi chuma kuposa anthu onse a m'mbuyo mwake.
neutral
koma nyanga za olungama zidzakwezedwa.
anger
Mumampempha modzichepetsa ndi motsitsa mawu (kuti): "Ngati atipulumutsa m'mazunzo awa, ndithudi tidzakhala mwa othokoza."
neutral
Koma Yesu ali padzikoli analamula kuti: "Lekani kuweruza poona maonekedwe akunja, koma muziweruza ndi chiweruzo cholungama."
anger
Iye anawayika chitonzo chamuyaya.
disgust
Kenaka anawapatsa ulamuliro kulakhula ngati kuti ndi mwini wake akulakhual.
anger
"E inu ana a Israyeli! kumbukirani chisomo Changa chomwe ndidakudalitsani nacho, ndipo kwaniritsani pangano Langa Nanenso ndikwaniritsi pangano lanu.
neutral
Ndipo sadzapeza mthandizi ndi mtetezi kupatula Allah.
neutral
Bambo wako sadali munthu woipa, ngakhalenso mayi wako sadali wachiwerewere."
disgust