Chichewa
stringlengths
10
500
emotion
stringclasses
7 values
Iwo adzabwera ndi kuona ulemerero wanga.
joy
Kodi Iye amene anapanga diso sangathe kuona?
surprise
Mitima yawo njokhazikika; sadzachita mantha.
fear
"Pamene mudalilandira (bodzalo) ndi malirime anu ndi kumanena ndi milomo yanu zomwe inu simukuzidziwa, ndipo mumaganizira kuti ndi chinthu Chochepa pomwe icho kwa Allah ndi chinthu chachikulu.
disgust
Ndipotu ananena kuti: "Ali kuti Mulungu wa chiweruzo?"
surprise
"Koma pamene adawadzera ndi zisonyezo zathu, basi iwo adali kuziseka.
disgust
Ife tawaika iwo mwamsanga ndipo tsopano sitingathe kugwira ntchito popanda iwo ."
neutral
"Ndithudi, amene sakhulupirira, chuma chawo ngakhale ana awo, sizidzawathandiza chilichonse kwa Allah.
anger
A baristas anali otanganidwa kwambiri kuti angakudziweni.
sadness
Kodi sadayende (iwo osakhulupirira) pa dziko nkuona momwe mathero a oipa omwe adalipo patsogolo pawo (momwe adalili)?
neutral
Ndithudi yemwe mudzamulowetse ku moto, ndiye kuti mwamuyalutsa, ndipo sipadzakhala athandizi kwa ochita zoipa.
disgust
Ndimafuna kukudziwitsani momwe Mulungu wagwiritsira ntchito SGS m'moyo wanga.
neutral
mulu wosagwirizana kapena mulu umene umakhala pa kanjedza pambuyo pa kuyanika;
neutral
Koma iyeyo akadzafika, mzimu wa choonadi, adzakutsogolerani m'choonadi chonse."
neutral
Iye Ndiye amatsogolera ndi kuteteza anthu omvera.
neutral
Ndi mzere wolunjika kwa Lady wathu.
neutral
"Ndipo moyo uwu wa pa dziko lapansi suli kanthu, koma chibwana ndi masewera.
joy
Ikhali ndjira ibodzi basi yakuti abweresa anthu kwa Mulungu.
neutral
"Choncho Allah adawalawitsa kunyozeka pa moyo wa pa dziko lapansi; koma ndithu chilango cha tsiku la chimaliziro nchachikulu zedi (kuposa chilango cha m'dziko lapansi) akadakhala akudziwa!
disgust
Ngati zili choncho, athandizeni kugwira ntchito zawozo mpaka mudzaone kuti angathe kugwira ntchitozo paokha.
neutral
"Kodi sayendayenda pa dziko kuti akhale ndi mitima (yanzeru) yowazindikiritsa ndi makutu omvera?
neutral
Tsopano ine ndiribe kumvera yemweyo ana a nyimbo CD mobwerezabwereza mu galimoto yanga.
neutral
Iye anati: "Osangalala ndinu, amene mukulira tsopano, chifukwa mudzaseka."
sadness
Kodi ifeyo timakhulupiriradi zimenezo? - Ngati timatero, ndiye kuti tidzapitiriza kuphunzira kwa Mphunzitsi Waluso tsiku lililonse, ndiponso tidzachita zimene amanena.
neutral
"Ndipo ngati adali mmodzi wa anthu akudzanja lamanja,
neutral
Tom ndi abwenzi ena analowa kudziwa Sisters:
neutral
"Ndipo ngati atatsimikiza kulekana, ndithudi Allah Ngwakumva, Ngodziwa.
neutral
Choncho, n'zodziwikiratu kuti anthu omwe amachiritsa mozizwitsa masiku ano mphamvu zawo zingachokere kwina, osati kwa Mulungu.
surprise
Limenelo ndilo tanthauzo la zomwe sudathe kupirira nazo."
neutral
napewa zimene Iye wamuletsa kuzichita,
neutral
Mdierekezi mwiniwake wasandulika Mulungu... pafupifupi.
disgust
Kuwonjezera pamenepo, ngakhale kuti ndi zoona kuti Mulungu sasintha, zofuna zake nthaŵi zina zimasintha.
neutral
""Ngati munyoza (kulandira chimene ndakuuzani palibe vuto kwa ine); ndithu ndafikitsa kwa inu chimene ndatumidwa.
anger
Motero kwa iwowo, Yobuyo sakanabwereranso kunyumba kwake kapenanso kudziwidwanso, kufikira nthawi imene Mulungu anaika.
anger
Chifukwa chake ndikuganiza kuti ku South Africa (ndi ku Brazil nakonso) izi ziyenera kukonzedwa.
neutral
(Iwe, Mneneri (SAW), zomwe Zikuvumbulutsidwa) Mdzina la Mbuye Wako yemwe adalenga (zolengedwa Zonse).
neutral
Mawu a alendo angamveke kudzera mwa anthu amene timayanjana nawo.
neutral
"Ndipo ngati mutaterezuka (kuchimwa) pambuyo pokudzerani zisonyezo (za Allah) zoonekera poyera, dziwani kuti Allah Ngwamphamvu zoposa; Ngwanzeru zakuya.
neutral
"Koma tawabweretsera choonadi; ndithu iwo ngabodza (potsutsana ndi choonadicho).
anger
"Kodi osakhulupirira anuwa ndi abwino kuposa iwo (kotero kuti sadzaonongedwa)?
surprise
Ndipo pamene akufika pafupi, izi ndizo zimene akuona.
neutral
Ndikufuna kuwonetsanso mavidiyo a Japan XXX.
joy
Adzakhala mʼdziko lawo, limene ndinalipereka kwa mtumiki wanga Yakobo.
neutral
Akadanena: "Tsoka kwa ife ndithu tidali osalungama."
disgust
Iye anati: "Nyumba yathu ndi katundu yense zinawonongeka ndipo abale anga ambiri anafa."
sadness
kuti: "Lowani ku moto limodzi ndi olowa
neutral
"Amene adalenga thambo zisanu ndi ziwiri mosanjikana (kapena zolingana mkalengedwe kake).
neutral
"Kodi pali chinachake cholakwika ndi mphete yanga?"
fear
Ndipo atafuna angakuchotseni (nthawi imodzi) ndikubweretsa zolengedwa zina zatsopano.
neutral
Koma aliyense amene amaloŵa m'kuunika kwa Mawu a Mulungu angathe kusintha.
neutral
Ndipo zamoyo zinai zinati, Amen.
disgust
Iye anasonyeza kuti Mulungu amaveka maluwa akutchire ndipo anati: "Kodi iye sadzakuvekani kuposa pamenepo, achikhulupiriro chochepa inu?
disgust
Musamaope munthu aliyense, pakuti chiweruzo ndi cha Mulungu.
fear
Tsiku lililonse tinaphunzira kanthu kena katsopano ponena za zolinga za Mulungu.
neutral
"Lowani ku Munda wamtendere, inu ndi akazi anu musangalatsidwa.
neutral
ndi kutambasula mapiko ake kupita kummwera?
neutral
"Ndipo Edda ya amene asiya kudwala kumwezi mwa akazi anu chifukwa cha kukula, ngati mukukaika (nthawi ya Edda yawo), Edda yawo ndi miyezi itatu.
neutral
"Eti akukufunsa: "Kodi nzoona izo (zimene ukunena)?"
neutral
yela selasa cuti maulidur rasul,..
neutral
Wanthu omwe ambacita bzakuipa an'dzabvumizidwa lini kukhala m'Paraizo.
neutral
"Ndipo tidawazindikiritsa ana a Israyeli m'bukulo, kuti: "Ndithu inu muononga pa dziko kawiri, ndipo mudzapyola malire pochita zoipa, kupyola malire kwakukulu.
disgust
Mbwenye khala diso yako ndi yakuipa, manungo ako onsene anakhala cidima.'
neutral
Ndipo iwo ananena naye, Kodi tikapita ife ndi kugula mikate ya pa marupiya atheka mazana awiri, ndi kuwapatsa kudya?
anger
Ndipo amene aphedwa panjira ya Allah, ntchito yawo sadzaipititsa pachabe.
sadness
Amen, Ndikukuuzani, ngati chizindikiro chidzaperekedwa kwa m'badwo uno!"
neutral
Ndithu ine ndaitanira anthu anga (ku chikhulupiliro) usiku ndi usana (popanda kufooka)."
neutral
Ngati simunamulandire Yesu monga Ambuye ndi Mpulumutsi wanu, simungatero tsopano lino?
neutral
"Kodi Wanzeru ndi Womvetsa Zinthu Ndani Pakati pa Inu?"
neutral
amuna ngati mabere akulu okha;
neutral
"Yemwe adzapewetsedwe ku chilangocho tsiku limenelo, ndiye kuti wamchitira chifundo; kumeneko nkupambana kowonekera.
neutral
Ndipo Iye adzatiphunzitsa njira zake, ndipo ife tidzayenda m'njira zakezo.
neutral
Anthu ake adamuuza: "Usanyade; ndithu Allah sakonda onyada."
anger
" (Iye) adati: "Kodi mukudziwa zomwe mudamchitira Yûsuf ndi m'bale wake pamene inu mudali mu umbuli?"
anger
"Ndipo tidawathangata (powagonjetsera adani awo), ndipo iwo adali opambana.
neutral
aneneri ena onse sitinaonepo kuwala kwa tsiku kuyambira iwo anapita mapazi asanu kwambiri ....
neutral
Ndipo mzimenezi chowonadi chakufika ndi ulaliki komanso chikumbutso kwa okhulupilira."
neutral
zokhazokhazi (Luti) adati: "E
neutral
Ndithudi, Allah adzawasonkhanitsa achiphamaso ndi osakhulupirira onse m'moto wa Jahannam.
disgust
Ndidzamva kufuula kwawo nadzawapulumutsa.
neutral
"" (Koma) boma singatikakamize mkazi kufa ngati iye wofuna kupulumutsa moyo wake.""
disgust
Ndipo ndidzampatsa iye mwana wamkazi pakati pa akazi, kuti kuwapasula.
neutral
Komabe, iye amene chakunyansani adzasenza chiweruzo, amene angakhale.
fear
mu nyumba ya mtumiki wake Davide.
disgust
ya amene Adalipo patsogolo pawo,
neutral
(Tikuonongani monga tidawaonongera iwo; koma) iwo adali ndi nyonga zambiri kuposa inu; adalinso ndi chuma chambiri ndi ana ambiri kuposa inu.
neutral
"Kudzanenedwa: "Lowani makomo a ku Jahannam; mukakhalitse mmenemo (nthawi yaitali)."
anger
Iye ananena kuti: "Mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake."
neutral
"Ndipo (akumbutse) tsiku lomwe tidzawasonkhanitsa onse pamodzi; kenako tidzati kwa omwe adali kuphatikiza (Allah ndi mafano): "Ali kuti aphatikizi anu aja omwe munkati ngothandizana ndi Allah?"
neutral
Koma satana adamuiwalitsa kumkumbutsa bwana wake.
disgust
Amene Anakonza ndi Best kwa Inu?
neutral
" (Ibrahim) adapita mozemba ku mafano awo, ndipo adawauza (mwachipongwe:) "Bwanji simukudya (chakudya chomwe chaikidwa patsogolo panupo)?"
fear
Solomo anapempha nzeru, chonde mafumu pemphani nzeru.
neutral
Choncho ndiwalembera (kuti mtendere umenewu udzakhale wawowawo pa tsiku lachimaliziro) amene akupewa (zoletsedwa) ndi kumapereka Zakaat, ndi kumakhulupirira zizindikiro Zathu;"
neutral
Ndithudi, amibadwo yoyamba ndi mibadwo yomaliza (omwe inu muli m'gulu lawo),
neutral
Mulungu monga tate amakhala m'maso a nzeru.
neutral
"Ndipo akauzidwa kuti: "Opa Allah," Akugwidwa ndi mwano womupititsa ku machimo, choncho Jahannam ikukwana kwa iye (kuwuchotsa mwano wakewo).
fear
Ndipo ena a inu amapatsidwa imfa asadaifike (nthawi ya ukalamba) nkuti muifikire nthawi imene yaikidwa; (zoterezi nkuti inu) mukhale ndi nzeru.
neutral
"Akuluakulu a mwa anthu ake omwe sadakhulupirire adanena: "Ife tili kukuona kuti uli mu uchidzete, ndipo ife tikukuganizira kuti ndiwe m'modzi wa a bodza."
neutral
"Akukufunsa (Asilamu) chomwe chaloledwa kwa iwo (kudya).
neutral
Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika ndi Woona."
neutral