Chichewa
stringlengths
10
500
emotion
stringclasses
7 values
Kukanidwa alibe phindu pa tsiku limenelo.
neutral
Ndipo aliyense sadziwa chomwe apeze mawa; (chabwino kapena choipa); ndiponso sadziwa aliyense kuti ndi dziko liti adzafera.
neutral
""Kodi mukudabwa kukudzerani ulaliki wochokera kwa Mbuye wanu kudzera mwa munthu wa mwa inu, (yemwe wadza) kuti akuchenjezeni ndi kuti muope (Allah), ndikutinso muchitiridwe chifundo?"
surprise
Inu sadzamva ana akuseka ndi kusewera mu Gehena, chifukwa palibe ana mu gehena.
disgust
Ndipo mwa inu amene akhalepo (pa mudzi) m'mweziwu, asale.
neutral
Ndiyeno anayamba kuuzana kuti: "Sitili kuchita bwino ife; tsiku lino ndilo tsiku la uthenga wabwino."
sadness
Zimenezo nchifukwa chakuti iwo adatsutsa zizindikiro Zathu ndipo anali osazilabadira.
disgust
Koma angakhale akukondabe Mulungu mumtima mwawo.
neutral
Aleke asangalale (ndi zoipa zawozo); posachedwa adzadziwa.
joy
mau powerenga Quràn, ndipo mosakhala m'menemo adzanong'ona powerenga.
neutral
Iye alonga: 'Iwo ndiwo mbumba yakuipa yakuti nkhabe bvera miyambo yanu.
anger
Ndipo iye ndi wopunduka diso lakumanja,
neutral
Tiyeni timgulitse iye kwa Aismayele, tisasamulire iye manja; chifukwa ndiye mbale wathu, thupi athu.
anger
mkazi wopanda ana, ngati mtengo wopanda nthambi;
disgust
Mulungu adati kwa Yobu, "Kodi udali kuti pamene ine ndinkayika madziko a dziko lapansi?
neutral
ku chilango cha tsiku limenelo ndi ana ake.
disgust
ndi kuti ukawayankhe zoona amene akutumawo?
neutral
Lero ndi tsiku lomwe muyenera kuyendera San Marino: The ...
neutral
"Ndipo mumpingo uliwonse tidzatulutsa mboni (yawo yowaikira umboni), ndipo tidzawauza: "Bwerani ndi umboni wanu."
neutral
Komatu nyumba ya chimaliziro idzawakhalira bwino amene akuopa (Allah).
joy
Ngati ukundiona ine kuti ndili ndi chuma chochepa ndi ana ochepa kuposa iwe (koma sindisiya kutamanda Allah)."
neutral
Ndipo amene angamphatikize Allah, ndithudi, wadzipekera uchimo waukulu.
disgust
"Sadzalawa imfa mmenemo, kupatula imfa yoyamba ija; ndipo adzawateteza kuchilango cha Jahena,
sadness
"Ndipo woipa adzauona moto (panthawi imeneyo) ndikutsimikiza kuti iwo alowa m'menemo.
sadness
"Kodi nchiyani chakupezani (kuti muweruze mopanda chilungamo); nanga mukuweruza bwanji (zimenezi)?
neutral
Kodi wadya zipatso za mtengo uja umene ndinakulamula kuti usadye? "
disgust
Sindinamvepo za inu anyamata, Ndinu ndani padziko lapansi?
surprise
Kodi sindiyenera kumvera chisoni mzinda waukulu ngati uwu?"
sadness
Koma Allah akunena choona; Iye akuongolera ku njira yoongoka.
neutral
Ambiri anazindikira kuti iye ankaphunzitsa choonadi ndipo "anakhala okhulupirira."
neutral
Ndipo adzawalowetsa m'minda yomwe pansi pake pakuyenda mitsinje, adzakhala m'menemo muyaya.
neutral
Tsopano zakhala ngati nyumba yachiwiri, ndimakonda kukakhala ku Dubai.
joy
"Ndipo musakhale monga aja amene adagawikana nasiyana pambuyo powadzera zisonyezo zoonekera poyera (zowaletsa kutero).
neutral
"Ngati atafuna angakuchotseni ndi kubweretsa zolengedwa zatsopano.
neutral
Ndipo kotero muwaike iwo pansi - ndipo mochuluka kwambiri.
neutral
Akanachokanso, mwina si bwenzi pano ndili m'gulu la Yehova."
neutral
Koma akadachita zomwe auzidwa, zikadakhala zabwino kwa iwo.
neutral
Kodi n'ciyani comwe cidacitika pomwe Salomau alibe kubvera cenjezo la Mulungu?
fear
Ndipo nyumba iliyonse yomwe apezako wampatuko, aziigwetsa."
anger
" (Iwo) adati: "Ndithu ife kwa Mbuye wathu ngobwerera."
neutral
"Ndipo tidampulumutsa iye ndi Luti kupita ku dziko lomwe tidalidalitsa ku zolengedwa.
joy
"Kuti achitsimikizire choonadi ndi kulichotsa bodza; ngakhale zikuwaipira anthu oipa.
disgust
Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m'kamwa mwake."
neutral
Ale anaibva, anapulumuka.
neutral
Anthu akhoza kutiuza kuti: "Anthufe timafunika kusangalala ndi moyo.
joy
Adalitsike Yehova, amene wapumulitsa anthu ake Israyeli, monga mwa zonse adalonjeza: sanataya mawu amodzi m'zonse zabwino zomwe adalonjeza ndi dzanja la Mose mtumiki wake.
neutral
Choncho padziko panali magulu a anthu awiri; omwe anali kupembedza Allah Subhaanah wa Ta'ala, ndi ena omwe anali kupitiriza kupembedza mafano.
neutral
Choncho pamene adamdzera, (mneneri Shuaib) ndikumulongosolera nkhani, adati: "Usaope; wapulumuka kwa anthu oipa."
fear
Pamene anali kuvutika, sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye amene amaweruza molungama."
fear
Iye anati: "Ndinatsatira malangizo amene akulu anandipatsa ndipo ndinayamba moyo wosalira zambiri.
neutral
Ngati ndati ayi, ndiye kuti ndili wotanganidwa.
sadness
Mtima wake udzakwezeka, ndipo adzagwetsa anthu masauzande ambiri; koma sadzakhala wamphamvu. "
sadness
Koma masiku ano tili pafupi kwambiri ndi nthawi imene Mulungu akufuna kukwaniritsa zimene analonjeza.
joy
"Ndipo ndithu Ife ndi Wokhoza kukuonetsa (chilango) chimene tikuwalonjeza.
neutral
"Kenako akadzafuna adzamuukitsa (pambuyo pa imfa).
disgust
Ine ndidzalanga dziko chifukwa zoipa zake, oipa chifukwa cha kusaweruzika kwawo.
anger
Palibe kumene kuli malipiro anga koma kwa Mbuye wa zolengedwa."
neutral
Ndipo m'zimenezi choonadi chakufika ndi ulaliki ndiponso chikumbutso kwa okhulupirira.
neutral
Kwenikweni, zomwe amaphunzitsa ndi chowonadi cha Mulungu mpaka atatiuza mosiyana.
neutral
Iwowo ndiomwe Allah sadafune kuyeretsa mitima yawo.
neutral
Mukabisale kumeneko masiku atatu, mpaka iwo atabwerako, kenako muzikapita kwanu."
neutral
Ndithu m'zimenezi muli zisonyezo kwa anthu anzeru.
neutral
Ndipo taikonza Jahannam kukhala ndende ya osakhulupirira."
neutral
Mulungu anapanga pangano ndi ife.
neutral
Bambo wako sadali munthu woipa, ngakhalenso mayi wako sadali wachiwerewere,"
disgust
"Amene amaimilira kupemphera napereka chimene tawapatsa, (pa njira ya Allah, ndikuthandiza ovutika).
neutral
owongoka (ofotokoza za choona).
neutral
Ndipo anapitadi kumwamba mu mtambo adani awo aja akuwaona.
anger
Komanso oitanidwa aja, amene ali osankhidwa mwapadera ndi okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi."
neutral
Choncho, adzaiitana koma siidzawayankha; ndipo tidzaika chionongeko pakati pawo (ndipo sadzakumananso).
sadness
Iye anati: "Inu ndinu mchere wa dziko lapansi.
disgust
Anadzipangira yekha kudzathandiza tsiku lina, ngati angathe.
neutral
Ine sinditsata china koma zomwe zikuvumbulutsidwa kwa ine."
neutral
Adzabwera ndi mthenga wa pangano amene mukumuyembekezera mosangalala."
neutral
"Kwa Iye ndiko kuli (kuvomera) pempho lachoonadi.
neutral
Nthaŵi zonse angelo anali kudziŵa kumene Paulo anali, ndipo anamuthandiza.
neutral
"Chifukwa chakuchita kwawo zoipa, awo Ayuda, tidaletsa kwa iwo zinthu zabwino (zakudya) zomwe zidali zovomerezeka kwa iwo; ndiponso chifukwa cha kutsekereza kwawo anthu ambiri kuyenda panjira ya Allah.
disgust
Koma chifukwa cha osankhidwawo, masikuwo adzafupikitsidwa."
neutral
Kapena ali nawo makutu omvelera?
neutral
Solomo anali munthu wolemera kwambiri.
neutral
Mukuona bwanji ngati ndili ndi umboni wowonekera wochokera kwa Mbuye wanga, ndipo nkundipatsa rizq labwino (lahalali) lochokera kwa Iye, (ndisiye zimenezi ndi kusankha njira yokhota)?
neutral
Inu Munafuna kuzizindikiritsa Nokha kwa wanthu; choncho, kupyolera mwa liu lapakamwa panu munadzetsa chilengedwe ndi kupanga m'mwamba.
neutral
Iwo ayenera kuti anaphunzitsa mwana wawo, dzina lake Samisoni, chilamulo cha Mulungu ndipo zotsatira zake zinali zabwino.
neutral
Ndipo wawakonzera minda yomwe mitsinje ikuyenda pansi (ndi pasogolo) pake, adzakhala m'menemo muyaya.
neutral
Ndipo adzabwerera kwa anthu ake
neutral
Ndithu Allah ndi mwini kuthekera, komanso muwongoli ku njira ya chiongoko.
neutral
Uthenga wabwino wa Ufumu ukulalikidwa padziko lonse lapansi monga mmene Yesu ananenera.
neutral
Ndikuganiza kuti ukunena zowona, Tim!
joy
Mose ankakonda Mulungu komanso aisiraeli anzake.
disgust
Chifukwa chake, anthu ammudziwo adampatsa dzina losavuta ndi lalifupi - Philip Goldson.
neutral
" (Iwo) adati: "Kodi watidzera kuti utichotse ku zimene tidawapeza nazo makolo athu kuti ukulu ukhale wa inu awiri m'dzikoli?
neutral
Koma yemwe akwaniritse Zomwe adalonjeza kwa Mulungu, amulipira malipiro aakulu.
neutral
Mukuona bwanji ngati ndili ndi chisonyezo choonekera chochokera kwa Mbuye wanga (chosonyeza kuona kwa zimenezi), nandipatsanso chifundo chochokera kwa Iye.
neutral
Inatengedwanso ndi Nigerian Bulletin.
neutral
"Pamene m'bale wawo Swalih adawauza kuti: "Kodi simuopa (Allah)?"
fear
Anthu ake adamuuza: "usanyade, ndithu Allah sakonda onyada."
anger
Koma pamene Aigupto analondola Aisrayeliwo m'nyanjamo, Mulungu anabwezeretsa madziwo m'malo mwake.
anger
Ndipo adzafika kwa anthu n'kumawaitanira anthuwo ku zofuna zake,
anger
Uku iwo akuyang'ana zomwe amawachitira Okhulupirira, (pootchedwa ndi moto).
disgust
Bukuli lidzasintha malingaliro anu. "
neutral